Mika 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zonse zimene munanena kwa Yakobo zinali zoona ndipo Abulahamu munamusonyeza kukoma mtima kosatha. Ifenso mudzatichitira zomwezo chifukwa n’zimene munalonjeza makolo athu kalekale.+ Luka 1:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Kuchitira chifundo makolo athu akale ndi kukumbukira pangano lake loyera,+
20 Zonse zimene munanena kwa Yakobo zinali zoona ndipo Abulahamu munamusonyeza kukoma mtima kosatha. Ifenso mudzatichitira zomwezo chifukwa n’zimene munalonjeza makolo athu kalekale.+