Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, monganso mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Komanso mbewu yako idzalanda chipata* cha adani ake.+

  • Salimo 105:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Wakumbukira pangano limene anapangana ndi Abulahamu,+

      Ndi lonjezo limene analumbira kwa Isaki,+

  • Luka 1:72
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 72 Kuchitira chifundo makolo athu akale ndi kukumbukira pangano lake loyera,+

  • Machitidwe 3:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Inu ndinu ana+ a aneneri ndi a pangano limene Mulungu anapangana ndi makolo anu akale. Iye anauza Abulahamu kuti, ‘Kudzera mwa mbewu yako mabanja onse a padziko lapansi adzadalitsidwa.’+

  • Aheberi 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu,+ analumbira pa dzina lake+ chifukwa panalibe wina wamkulu kwa iye amene akanamulumbirira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena