Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 11:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndiyeno mthengayo anauza Davide kuti: “Amunawo anakula mphamvu kuposa ife, moti anatuluka kudzamenyana nafe kuthengo, koma tinayesetsa kuwapanikiza mpaka kuchipata cha mzinda.

  • Salimo 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Tandipempha,+ ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kukhala cholowa chako,+

      Ndikupatsa dziko lonse lapansi kukhala lako.+

  • Danieli 2:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 “M’masiku a mafumu amenewo,+ Mulungu wakumwamba+ adzakhazikitsa ufumu+ umene sudzawonongedwa ku nthawi zonse.+ Ufumuwo sudzaperekedwa kwa mtundu wina uliwonse wa anthu,+ koma udzaphwanya ndi kuthetsa maufumu ena onsewo,+ ndipo udzakhalapo mpaka kalekale.+

  • Aheberi 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Chotero, popeza kuti “ana” amenewo onse ndi amagazi ndi mnofu, iyenso anakhala wamagazi ndi mnofu.+ Anachita izi kuti kudzera mu imfa yake,+ awononge+ Mdyerekezi,+ amene ali ndi njira yobweretsera imfa.+

  • Chivumbulutso 11:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mngelo wa 7 analiza lipenga+ lake. Ndipo kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana, akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake.+ Iye adzalamulira monga mfumu kwamuyaya.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena