Salimo 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anthu onse okhala kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova ndi kubwerera kwa iye.+Ndipo mafuko onse a anthu a mitundu ina adzagwada pamaso panu.+ Salimo 110:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova adzatambasula ndodo+ yako yachifumu yamphamvu kuchokera m’Ziyoni+ ndi kunena kuti:“Pita ukagonjetse anthu pakati pa adani ako.”+ Mateyu 25:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mitundu yonse ya anthu idzasonkhanitsidwa kwa iye+ ndipo adzalekanitsa+ anthu,+ mmene m’busa amalekanitsira nkhosa ndi mbuzi.
27 Anthu onse okhala kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova ndi kubwerera kwa iye.+Ndipo mafuko onse a anthu a mitundu ina adzagwada pamaso panu.+
2 Yehova adzatambasula ndodo+ yako yachifumu yamphamvu kuchokera m’Ziyoni+ ndi kunena kuti:“Pita ukagonjetse anthu pakati pa adani ako.”+
32 Mitundu yonse ya anthu idzasonkhanitsidwa kwa iye+ ndipo adzalekanitsa+ anthu,+ mmene m’busa amalekanitsira nkhosa ndi mbuzi.