Ezekieli 34:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Koma inu nkhosa zanga, imvani zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena. Iye wanena kuti: “Ine ndidzaweruza mwachilungamo pakati pa nkhosa ndi nkhosa inzake komanso pakati pa nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+ Mateyu 13:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndi mmenenso zidzakhalire pa mapeto a nthawi* ino: Angelo adzapita n’kukachotsa oipa+ pakati pa olungama+
17 “‘Koma inu nkhosa zanga, imvani zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena. Iye wanena kuti: “Ine ndidzaweruza mwachilungamo pakati pa nkhosa ndi nkhosa inzake komanso pakati pa nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+
49 Ndi mmenenso zidzakhalire pa mapeto a nthawi* ino: Angelo adzapita n’kukachotsa oipa+ pakati pa olungama+