Salimo 72:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo adzakhala ndi anthu omugonjera kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,+Komanso kuchokera ku Mtsinje*+ kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+ Aheberi 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumapeto kwa masiku ano,+ iye walankhulanso kwa ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamuika kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Kudzera mwa iyeyu, Mulungu analenga+ nthawi* zosiyanasiyana. Chivumbulutso 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mngelo wa 7 analiza lipenga+ lake. Ndipo kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana, akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake.+ Iye adzalamulira monga mfumu kwamuyaya.”+
8 Ndipo adzakhala ndi anthu omugonjera kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,+Komanso kuchokera ku Mtsinje*+ kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+
2 Kumapeto kwa masiku ano,+ iye walankhulanso kwa ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamuika kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Kudzera mwa iyeyu, Mulungu analenga+ nthawi* zosiyanasiyana.
15 Mngelo wa 7 analiza lipenga+ lake. Ndipo kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana, akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake.+ Iye adzalamulira monga mfumu kwamuyaya.”+