Agalatiya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma nthawi itakwana,+ Mulungu anatumiza Mwana wake,+ amene anadzabadwa kwa mkazi+ ndipo anadzakhala pansi pa chilamulo.+ 1 Petulo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anali kufufuza nyengo+ yake kapena mtundu wa nyengo imene mzimu+ umene unali mwa iwo unali kuwasonyeza yokhudzana ndi Khristu.+ Mzimuwo unali kuchitira umboni za masautso a Khristu+ ndi za ulemerero+ wobwera pambuyo pake. 1 Petulo 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye anadziwikiratu dziko lisanakhazikitsidwe,+ koma anaonekera pa nthawi ya mapeto chifukwa cha inuyo,+
4 Koma nthawi itakwana,+ Mulungu anatumiza Mwana wake,+ amene anadzabadwa kwa mkazi+ ndipo anadzakhala pansi pa chilamulo.+
11 Anali kufufuza nyengo+ yake kapena mtundu wa nyengo imene mzimu+ umene unali mwa iwo unali kuwasonyeza yokhudzana ndi Khristu.+ Mzimuwo unali kuchitira umboni za masautso a Khristu+ ndi za ulemerero+ wobwera pambuyo pake.
20 Iye anadziwikiratu dziko lisanakhazikitsidwe,+ koma anaonekera pa nthawi ya mapeto chifukwa cha inuyo,+