Yesaya 65:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Pakuti ndikulenga kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano.+ Zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso+ ndipo sizidzabweranso mumtima.+ Yesaya 66:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 chifukwa mudzayamwa bere lake ndipo mudzakhuta kutonthoza kwake. Komanso mudzayamwa mkaka wake ndipo mudzasangalala kwambiri ndi bere lake laulemerero.+
17 “Pakuti ndikulenga kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano.+ Zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso+ ndipo sizidzabweranso mumtima.+
11 chifukwa mudzayamwa bere lake ndipo mudzakhuta kutonthoza kwake. Komanso mudzayamwa mkaka wake ndipo mudzasangalala kwambiri ndi bere lake laulemerero.+