Salimo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tandipempha,+ ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kukhala cholowa chako,+Ndikupatsa dziko lonse lapansi kukhala lako.+ Yohane 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zonse zimene Atate ali nazo ndi zanga.+ N’chifukwa chake ndikunena kuti adzalandira za ine ndi kuzilengeza kwa inu. Aroma 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero, ngati tili ana, tilinso olandira cholowa: Olandira cholowa a Mulungu, komanso olandira cholowa anzake+ a Khristu, malinga ngati tivutika+ naye limodzi kuti tikalandire ulemerero limodzi ndi iye.+
8 Tandipempha,+ ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kukhala cholowa chako,+Ndikupatsa dziko lonse lapansi kukhala lako.+
15 Zonse zimene Atate ali nazo ndi zanga.+ N’chifukwa chake ndikunena kuti adzalandira za ine ndi kuzilengeza kwa inu.
17 Chotero, ngati tili ana, tilinso olandira cholowa: Olandira cholowa a Mulungu, komanso olandira cholowa anzake+ a Khristu, malinga ngati tivutika+ naye limodzi kuti tikalandire ulemerero limodzi ndi iye.+