Mateyu 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atate wanga wapereka zinthu zonse kwa ine, ndipo palibe amene akum’dziwa bwino Mwana koma Atate+ okha, komanso palibe amene akuwadziwa bwino Atate koma Mwana yekha+ ndi aliyense amene Mwanayo wafuna kumuululira za Atatewo.+ Yohane 3:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atate amakonda Mwana wake+ ndipo anapereka zinthu zonse m’manja mwake.+ Yohane 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zonse zimene ndili nazo ndi zanu ndipo zanu zonse ndi zanga.+ Ine ndalemekezeka pakati pawo.
27 Atate wanga wapereka zinthu zonse kwa ine, ndipo palibe amene akum’dziwa bwino Mwana koma Atate+ okha, komanso palibe amene akuwadziwa bwino Atate koma Mwana yekha+ ndi aliyense amene Mwanayo wafuna kumuululira za Atatewo.+