Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 28:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Tsopano Yesu anayandikira ndi kulankhula nawo kuti: “Ulamuliro wonse+ waperekedwa kwa ine kumwamba ndi padziko lapansi.

  • Luka 10:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Atate wanga wapereka+ zinthu zonse kwa ine, ndipo palibe amene akum’dziwa bwino Mwana koma Atate okha. Komanso Atatewo+ palibe amene akuwadziwa bwino koma Mwana+ yekha ndiponso amene Mwanayo wakonda kuwaululira za Atatewo.”

  • Yohane 10:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 monga mmene zilili kuti Atate amandidziwa, inenso ndimawadziwa Atate.+ Chotero, ndipereka moyo wanga chifukwa cha nkhosazo.+

  • 1 Yohane 5:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tikudziwa kuti Mwana wa Mulungu anabwera,+ ndipo anatipatsa nzeru+ kuti timudziwe woonayo.+ Ndipo ife ndife ogwirizana+ ndi woonayo, kudzera mwa Mwana wake Yesu Khristu. Iyeyo ndiye Mulungu woona+ ndiponso wopereka moyo wosatha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena