Yohane 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 monga mmene zilili kuti Atate amandidziwa, inenso ndimawadziwa Atate.+ Chotero, ndipereka moyo wanga chifukwa cha nkhosazo.+
15 monga mmene zilili kuti Atate amandidziwa, inenso ndimawadziwa Atate.+ Chotero, ndipereka moyo wanga chifukwa cha nkhosazo.+