Afilipi 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zili choncho chifukwa inu munapatsidwa mwayi. Osati mwayi wokhulupirira+ Khristu wokha, komanso wovutika+ chifukwa cha iye. Akolose 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndikusangalala tsopano ndi masautso amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso kumbali yanga, ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira+ monga chiwalo cha thupi la Khristu, limene ndi mpingo.+
29 Zili choncho chifukwa inu munapatsidwa mwayi. Osati mwayi wokhulupirira+ Khristu wokha, komanso wovutika+ chifukwa cha iye.
24 Ndikusangalala tsopano ndi masautso amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso kumbali yanga, ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira+ monga chiwalo cha thupi la Khristu, limene ndi mpingo.+