Aefeso 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa chifukwa chimenechi, ine Paulo, ndine wandende+ mwa Khristu Yesu m’malo mwa inu, anthu a mitundu ina+ . . . Afilipi 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndachita zimenezi kuti ndim’dziwe komanso kuti ndidziwe mphamvu ya kuuka kwake kwa akufa.+ Kutinso ndigawane naye m’masautso+ ake, ndi kulolera kufa imfa monga yake.+
3 Pa chifukwa chimenechi, ine Paulo, ndine wandende+ mwa Khristu Yesu m’malo mwa inu, anthu a mitundu ina+ . . .
10 Ndachita zimenezi kuti ndim’dziwe komanso kuti ndidziwe mphamvu ya kuuka kwake kwa akufa.+ Kutinso ndigawane naye m’masautso+ ake, ndi kulolera kufa imfa monga yake.+