16 Akutero pamene akuyesa kutiletsa+ kulankhula kwa anthu a mitundu ina kuti angapulumutsidwe.+ Chotsatira chake n’chakuti, pochita zimenezi nthawi zonse akudzazitsa+ machimo awo. Koma tsopano mkwiyo wake wawafikira.+
17 Koma Ambuye anaima pafupi ndi ine+ ndi kundipatsa mphamvu,+ kuti kudzera mwa ine, ntchito yolalikira ichitidwe mokwanira, ndi kuti mitundu yonse ya anthu imve uthengawo.+ Ndiponso ndinapulumutsidwa m’kamwa mwa mkango.+