Luka 11:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 “Tsoka inu odziwa Chilamulo, chifukwa munalanda anthu kiyi yowathandiza kudziwa zinthu.+ Inuyo simunalowemo, ndipo ofuna kulowamo munawatsekereza!”+ Machitidwe 13:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Koma Ayuda+ anauza zoipa amayi otchuka amene anali opembedza Mulungu, komanso amuna olemekezeka a mumzindawo. Chotero iwowa anachititsa kuti Paulo ndi Baranaba ayambe kuzunzidwa,+ ndipo anawaponya kunja kwa mzinda wawo.
52 “Tsoka inu odziwa Chilamulo, chifukwa munalanda anthu kiyi yowathandiza kudziwa zinthu.+ Inuyo simunalowemo, ndipo ofuna kulowamo munawatsekereza!”+
50 Koma Ayuda+ anauza zoipa amayi otchuka amene anali opembedza Mulungu, komanso amuna olemekezeka a mumzindawo. Chotero iwowa anachititsa kuti Paulo ndi Baranaba ayambe kuzunzidwa,+ ndipo anawaponya kunja kwa mzinda wawo.