Afilipi 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Cholinga changa nʼchoti ndimudziwe komanso kuti ndidziwe mphamvu za amene anamuukitsa kwa akufa.+ Ndikufunanso kuti ndivutike ngati mmene iye anavutikira,+ mpaka kulolera kufa ngati mmene iye anafera.+ Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:10 Nsanja ya Olonda,2/15/2006, tsa. 22
10 Cholinga changa nʼchoti ndimudziwe komanso kuti ndidziwe mphamvu za amene anamuukitsa kwa akufa.+ Ndikufunanso kuti ndivutike ngati mmene iye anavutikira,+ mpaka kulolera kufa ngati mmene iye anafera.+