Aroma 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ngati tili ana, ndifenso olandira cholowa kuchokera kwa Mulungu. Koma ndifenso olandira cholowa+ anzake a Khristu, ngati tikuvutika naye limodzi+ kuti tikalandire naye ulemerero.+ 2 Akorinto 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi zonse timapirira tikamazunzidwa ngati mmene Yesu anachitira+ ndipo timachita zimenezi kuti moyo wa Yesu uonekerenso mwa ife.* Akolose 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano ndikusangalala ndi mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira monga chiwalo cha thupi la Khristu,+ limene ndi mpingo.+
17 Choncho ngati tili ana, ndifenso olandira cholowa kuchokera kwa Mulungu. Koma ndifenso olandira cholowa+ anzake a Khristu, ngati tikuvutika naye limodzi+ kuti tikalandire naye ulemerero.+
10 Nthawi zonse timapirira tikamazunzidwa ngati mmene Yesu anachitira+ ndipo timachita zimenezi kuti moyo wa Yesu uonekerenso mwa ife.*
24 Tsopano ndikusangalala ndi mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira monga chiwalo cha thupi la Khristu,+ limene ndi mpingo.+