Luka 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Musaope, kagulu ka nkhosa inu,+ chifukwa Atate wanu wavomereza kukupatsani Ufumu.+ Agalatiya 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiponso ngati muli ophunzira a Khristu, ndinudi mbadwa* za Abulahamu,+ olandira cholowa+ mogwirizana ndi lonjezolo.+
29 Ndiponso ngati muli ophunzira a Khristu, ndinudi mbadwa* za Abulahamu,+ olandira cholowa+ mogwirizana ndi lonjezolo.+