1 Akorinto 15:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Chifukwa matupi oti akhoza kuwonongekawa adzasintha nʼkukhala oti sangawonongeke.+ Ndipo matupi oti angafewa adzasintha nʼkukhala oti sangafe.+ Chivumbulutso 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amene wapambana pankhondo+ ndidzamulola kuti akhale ndi ine pampando wanga wachifumu,+ ngati mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu nditapambana pankhondo.
53 Chifukwa matupi oti akhoza kuwonongekawa adzasintha nʼkukhala oti sangawonongeke.+ Ndipo matupi oti angafewa adzasintha nʼkukhala oti sangafe.+
21 Amene wapambana pankhondo+ ndidzamulola kuti akhale ndi ine pampando wanga wachifumu,+ ngati mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu nditapambana pankhondo.