1 Yohane 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aliyense amene ndi mwana wa Mulungu amagonjetsa dziko.+ Ndipo chikhulupiriro chathu chatithandiza kugonjetsa dziko.+ Chivumbulutso 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa+ ndiponso chifukwa cha uthenga umene ankalalikira+ ndipo anali okonzeka kufa.+
4 Aliyense amene ndi mwana wa Mulungu amagonjetsa dziko.+ Ndipo chikhulupiriro chathu chatithandiza kugonjetsa dziko.+
11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa+ ndiponso chifukwa cha uthenga umene ankalalikira+ ndipo anali okonzeka kufa.+