1 Akorinto 15:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Pakuti chokhoza kuwonongekachi chidzavala kusawonongeka,+ ndipo chokhoza kufachi+ chidzavala kusafa. 2 Timoteyo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mawu awa ndi oona,+ akuti: Ndithudi, ngati tinafa naye limodzi, tidzakhalanso ndi moyo limodzi naye.+ Chivumbulutso 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Wopambana pa nkhondo+ ndidzamulola kukhala nane pampando wanga wachifumu,+ monga mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu+ nditapambana pa nkhondo.
53 Pakuti chokhoza kuwonongekachi chidzavala kusawonongeka,+ ndipo chokhoza kufachi+ chidzavala kusafa.
11 Mawu awa ndi oona,+ akuti: Ndithudi, ngati tinafa naye limodzi, tidzakhalanso ndi moyo limodzi naye.+
21 Wopambana pa nkhondo+ ndidzamulola kukhala nane pampando wanga wachifumu,+ monga mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu+ nditapambana pa nkhondo.