1 Yohane 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Onse amene ali ana+ a Mulungu amagonjetsa dziko.+ Ndipo tagonjetsa+ dziko ndi chikhulupiriro chathu.+ Chivumbulutso 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndipo amene wapambana pa nkhondo ndi kutsatira zochita zanga kufikira mapeto,+ ndidzamupatsa ulamuliro pa mitundu ya anthu.+ Chivumbulutso 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa,+ ndiponso chifukwa cha mawu a umboni wawo.+ Ndipo iwo sanaone kuti miyoyo yawo ndi yofunika,+ ngakhale pamene anali pa ngozi yoti akhoza kufa.
4 Onse amene ali ana+ a Mulungu amagonjetsa dziko.+ Ndipo tagonjetsa+ dziko ndi chikhulupiriro chathu.+
26 Ndipo amene wapambana pa nkhondo ndi kutsatira zochita zanga kufikira mapeto,+ ndidzamupatsa ulamuliro pa mitundu ya anthu.+
11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa,+ ndiponso chifukwa cha mawu a umboni wawo.+ Ndipo iwo sanaone kuti miyoyo yawo ndi yofunika,+ ngakhale pamene anali pa ngozi yoti akhoza kufa.