Chivumbulutso 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa,+ ndiponso chifukwa cha mawu a umboni wawo.+ Ndipo iwo sanaone kuti miyoyo yawo ndi yofunika,+ ngakhale pamene anali pa ngozi yoti akhoza kufa. Chivumbulutso 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako ndinaona chooneka ngati nyanja yagalasi+ yosakanikirana ndi moto. Ndipo amene anagonjetsa+ chilombo chija, chifaniziro chake,+ ndi nambala+ ya dzina lake, ndinawaona ataimirira pambali pa nyanja yagalasiyo,+ ali ndi azeze+ a Mulungu.
11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa,+ ndiponso chifukwa cha mawu a umboni wawo.+ Ndipo iwo sanaone kuti miyoyo yawo ndi yofunika,+ ngakhale pamene anali pa ngozi yoti akhoza kufa.
2 Kenako ndinaona chooneka ngati nyanja yagalasi+ yosakanikirana ndi moto. Ndipo amene anagonjetsa+ chilombo chija, chifaniziro chake,+ ndi nambala+ ya dzina lake, ndinawaona ataimirira pambali pa nyanja yagalasiyo,+ ali ndi azeze+ a Mulungu.