1 Yohane 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikulembera inu abambo+ chifukwa mukumudziwa iye amene wakhalapo kuyambira pa chiyambi.+ Ndikulembera inu anyamata chifukwa ndinu olimba+ ndipo mawu a Mulungu akhaladi mwa inu+ ndiponso mwagonjetsa woipayo.+
14 Ndikulembera inu abambo+ chifukwa mukumudziwa iye amene wakhalapo kuyambira pa chiyambi.+ Ndikulembera inu anyamata chifukwa ndinu olimba+ ndipo mawu a Mulungu akhaladi mwa inu+ ndiponso mwagonjetsa woipayo.+