Aheberi 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Pangano limene ndidzapangana ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa pangano loyamba lija ndi ili: Ndidzaika malamulo anga m’maganizo mwawo ndi kuwalemba m’mitima yawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo+ ndipo iwo adzakhala anthu anga,’+ watero Yehova. 2 Yohane 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Timakukondani chifukwa cha choonadi chimene chili mumtima mwathu,+ ndipo chidzakhalabe ndi ife mpaka muyaya.+ 3 Yohane 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinasangalala kwambiri pamene abale anabwera ndi kupereka umboni wa mmene ukupitira patsogolo m’choonadi, ndipo ndikusangalala chifukwa ukupitirizabe kuyenda m’choonadi.+
10 “‘Pangano limene ndidzapangana ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa pangano loyamba lija ndi ili: Ndidzaika malamulo anga m’maganizo mwawo ndi kuwalemba m’mitima yawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo+ ndipo iwo adzakhala anthu anga,’+ watero Yehova.
2 Timakukondani chifukwa cha choonadi chimene chili mumtima mwathu,+ ndipo chidzakhalabe ndi ife mpaka muyaya.+
3 Ndinasangalala kwambiri pamene abale anabwera ndi kupereka umboni wa mmene ukupitira patsogolo m’choonadi, ndipo ndikusangalala chifukwa ukupitirizabe kuyenda m’choonadi.+