Yeremiya 31:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Pangano+ limene ndidzapangane ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa masiku amenewo ndi ili:+ Ndidzaika chilamulo changa mwa iwo+ ndipo ndidzachilemba mumtima mwawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga,”+ watero Yehova. Zekariya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndithu ndidzawabweretsa, ndipo adzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo woona ndi wachilungamo.’”+ Aheberi 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Pangano limene ndidzapanga nawo pambuyo pa pangano loyamba lija ndi ili: Ndidzaika malamulo anga m’mitima yawo ndi kuwalemba m’maganizo mwawo,’ watero Yehova,”+
33 “Pangano+ limene ndidzapangane ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa masiku amenewo ndi ili:+ Ndidzaika chilamulo changa mwa iwo+ ndipo ndidzachilemba mumtima mwawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga,”+ watero Yehova.
8 Ndithu ndidzawabweretsa, ndipo adzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo woona ndi wachilungamo.’”+
16 “‘Pangano limene ndidzapanga nawo pambuyo pa pangano loyamba lija ndi ili: Ndidzaika malamulo anga m’mitima yawo ndi kuwalemba m’maganizo mwawo,’ watero Yehova,”+