Yeremiya 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo ngati udzalumbira+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wachoonadi+ ndi chilungamo,’+ pamenepo mitundu ya anthu idzapeza madalitso* kudzera mwa iye ndipo idzadzitama m’dzina lake.”+ Chivumbulutso 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aliyense wopambana pa nkhondo adzalandira zimenezi monga cholowa. Ineyo ndidzakhala Mulungu wake,+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+
2 Ndipo ngati udzalumbira+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wachoonadi+ ndi chilungamo,’+ pamenepo mitundu ya anthu idzapeza madalitso* kudzera mwa iye ndipo idzadzitama m’dzina lake.”+
7 Aliyense wopambana pa nkhondo adzalandira zimenezi monga cholowa. Ineyo ndidzakhala Mulungu wake,+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+