Deuteronomo 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Muziopa Yehova Mulungu wanu.+ Muzim’tumikira,+ kum’mamatira+ ndi kulumbira pa dzina lake.+ Yesaya 65:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero aliyense wofuna kudalitsidwa padziko lapansi adzadalitsidwa ndi Mulungu wokhulupirika.+ Aliyense wolumbira padziko lapansi adzalumbira pa Mulungu wokhulupirika,+ chifukwa masautso akale adzaiwalika ndipo sadzaonedwanso ndi maso anga.+
16 Chotero aliyense wofuna kudalitsidwa padziko lapansi adzadalitsidwa ndi Mulungu wokhulupirika.+ Aliyense wolumbira padziko lapansi adzalumbira pa Mulungu wokhulupirika,+ chifukwa masautso akale adzaiwalika ndipo sadzaonedwanso ndi maso anga.+