Deuteronomo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uziopa Yehova Mulungu wako+ ndi kum’tumikira,+ ndipo uzilumbira pa dzina lake.+ Yeremiya 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo ngati udzalumbira+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wachoonadi+ ndi chilungamo,’+ pamenepo mitundu ya anthu idzapeza madalitso* kudzera mwa iye ndipo idzadzitama m’dzina lake.”+ Yeremiya 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Ndiyeno anthu a mitundu ina akadzaphunzira njira za anthu anga ndi kulumbira m’dzina langa+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo!’ monga mmene iwo anaphunzitsira anthu anga kulumbira m’dzina la Baala,+ anthu a mitundu inawo adzakhazikika pakati pa anthu anga.+
2 Ndipo ngati udzalumbira+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wachoonadi+ ndi chilungamo,’+ pamenepo mitundu ya anthu idzapeza madalitso* kudzera mwa iye ndipo idzadzitama m’dzina lake.”+
16 “Ndiyeno anthu a mitundu ina akadzaphunzira njira za anthu anga ndi kulumbira m’dzina langa+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo!’ monga mmene iwo anaphunzitsira anthu anga kulumbira m’dzina la Baala,+ anthu a mitundu inawo adzakhazikika pakati pa anthu anga.+