Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 14:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Koma Abulamu anauza mfumu ya ku Sodomuyo kuti: “Ndikukweza manja anga kulumbira+ kwa Yehova Mulungu Wam’mwambamwamba, Amene anapanga kumwamba ndi dziko lapansi.

  • Deuteronomo 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Uziopa Yehova Mulungu wako+ ndi kum’tumikira,+ ndipo uzilumbira pa dzina lake.+

  • Deuteronomo 10:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Muziopa Yehova Mulungu wanu.+ Muzim’tumikira,+ kum’mamatira+ ndi kulumbira pa dzina lake.+

  • Oweruza 21:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsopano popeza kuti ife talumbira+ pali Yehova kuti sitiwapatsa ana athu aakazi kuti akhale akazi awo,+ tichita chiyani ndi anthu amene atsala opanda akaziwa?”

  • Yesaya 65:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Chotero aliyense wofuna kudalitsidwa padziko lapansi adzadalitsidwa ndi Mulungu wokhulupirika.+ Aliyense wolumbira padziko lapansi adzalumbira pa Mulungu wokhulupirika,+ chifukwa masautso akale adzaiwalika ndipo sadzaonedwanso ndi maso anga.+

  • Yeremiya 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndipo ngati udzalumbira+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wachoonadi+ ndi chilungamo,’+ pamenepo mitundu ya anthu idzapeza madalitso* kudzera mwa iye ndipo idzadzitama m’dzina lake.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena