Genesis 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kudzera mwa mbewu yako,+ mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso* ndithu chifukwa chakuti wamvera mawu anga.’”+ Salimo 72:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale.+Nthawi zonse pamene dzuwa latuluka, dzina lake lizitchuka,Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.*+Mitundu yonse ya anthu imutche wodala.+ Yeremiya 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo ngati udzalumbira+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wachoonadi+ ndi chilungamo,’+ pamenepo mitundu ya anthu idzapeza madalitso* kudzera mwa iye ndipo idzadzitama m’dzina lake.”+
18 Kudzera mwa mbewu yako,+ mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso* ndithu chifukwa chakuti wamvera mawu anga.’”+
17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale.+Nthawi zonse pamene dzuwa latuluka, dzina lake lizitchuka,Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.*+Mitundu yonse ya anthu imutche wodala.+
2 Ndipo ngati udzalumbira+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wachoonadi+ ndi chilungamo,’+ pamenepo mitundu ya anthu idzapeza madalitso* kudzera mwa iye ndipo idzadzitama m’dzina lake.”+