Salimo 45:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzatchula dzina lanu m’mibadwo yonse yam’tsogolo.+N’chifukwa chake mitundu ya anthu idzakutamandani mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya. Salimo 89:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mbewu yake idzakhala mpaka kalekale,+Ndipo mpando wake wachifumu udzakhala ngati dzuwa pamaso panga.+
17 Ndidzatchula dzina lanu m’mibadwo yonse yam’tsogolo.+N’chifukwa chake mitundu ya anthu idzakutamandani mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.
36 Mbewu yake idzakhala mpaka kalekale,+Ndipo mpando wake wachifumu udzakhala ngati dzuwa pamaso panga.+