Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Tsopano Aisiraeli inu, kodi Yehova Mulungu wanu akufuna kuti muzichita chiyani,+ koposa kuopa+ Yehova Mulungu wanu kuti muziyenda m’njira zake zonse,+ kukonda+ ndi kutumikira Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+

  • Deuteronomo 13:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Muzitsatira Yehova Mulungu wanu, muzimuopa, muzisunga malamulo ake, muzimvera mawu ake, muzim’tumikira ndi kum’mamatira.+

  • Salimo 34:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Opani Yehova, inu oyera ake,+

      Pakuti onse omuopa sasowa kanthu.+

  • Salimo 128:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 128 Wodala ndi aliyense woopa Yehova,+

      Amene amayenda m’njira za Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena