Yoswa 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso musayanjane ndi mitundu+ imene yatsala pakati panu. Musamatchule mayina a milungu yawo+ kapena kulumbirira pa milunguyo,+ ndipo musamaitumikire kapena kuigwadira.+ Zefaniya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzafafaniza anthu amene akugwadira khamu la zinthu zakuthambo pamadenga* a nyumba zawo,+ ndiponso amene akugwada ndi kulumbira+ kuti adzakhala okhulupirika kwa Yehova+ koma amakhalanso akulumbira m’dzina la Malikamu.+
7 Ndiponso musayanjane ndi mitundu+ imene yatsala pakati panu. Musamatchule mayina a milungu yawo+ kapena kulumbirira pa milunguyo,+ ndipo musamaitumikire kapena kuigwadira.+
5 Ndidzafafaniza anthu amene akugwadira khamu la zinthu zakuthambo pamadenga* a nyumba zawo,+ ndiponso amene akugwada ndi kulumbira+ kuti adzakhala okhulupirika kwa Yehova+ koma amakhalanso akulumbira m’dzina la Malikamu.+