Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 23:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiponso musayanjane ndi mitundu+ imene yatsala pakati panu. Musamatchule mayina a milungu yawo+ kapena kulumbirira pa milunguyo,+ ndipo musamaitumikire kapena kuigwadira.+

  • 1 Mafumu 11:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ndichita zimenezi chifukwa iwo andisiya ine+ n’kuyamba kugwadira Asitoreti+ mulungu wamkazi wa Asidoni, Kemosi+ mulungu wa Amowabu, ndi Milikomu+ mulungu wa ana a Amoni. Sanayende m’njira zanga mwa kuchita choyenera pamaso panga ndi kutsatira malamulo anga ndi zigamulo zanga monga anachitira Davide bambo a Solomo.

  • Yeremiya 49:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Ponena za ana a Amoni+ Yehova wanena kuti: “Kodi Isiraeli alibe ana aamuna, kapena kodi alibe wolandira cholowa? N’chifukwa chiyani Malikamu+ watenga Gadi+ kukhala cholowa chake? N’chifukwa chiyani anthu olambira Malikamu akukhala m’mizinda ya Isiraeli?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena