Salimo 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kusakaza kwa mdani kwatheratu tsopano,+Mizinda imene mwaifafaniza, nayonso yatheratu.+Dzina la mdani wanu silidzatchulidwanso.+
6 Kusakaza kwa mdani kwatheratu tsopano,+Mizinda imene mwaifafaniza, nayonso yatheratu.+Dzina la mdani wanu silidzatchulidwanso.+