Ekisodo 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Chilimikani ndi kuona chipulumutso cha Yehova chimene akuchitireni lero.+ Pakuti Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso, ndithu, simudzawaonanso.+ Salimo 34:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa,+Kuti dzina lawo lisatchulidwenso padziko lapansi.+
13 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Chilimikani ndi kuona chipulumutso cha Yehova chimene akuchitireni lero.+ Pakuti Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso, ndithu, simudzawaonanso.+
16 Nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa,+Kuti dzina lawo lisatchulidwenso padziko lapansi.+