Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Choncho pa tsiku limenelo Yehova anapulumutsa Isiraeli m’manja mwa Aiguputo,+ ndipo Isiraeli anaona Aiguputo atafa m’mphepete mwa nyanja.+

  • Ekisodo 15:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Amizidwa ndi madzi amphamvu.+ Amira pansi pa nyanja ngati mwala.+

  • Salimo 136:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Amenenso anakutumulira Farao ndi gulu lake lankhondo m’Nyanja Yofiira:+

      Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+

  • Miyambo 16:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Yehova anapanga chilichonse n’cholinga,+ ndipo ngakhale woipa anamusungira tsiku loipa.+

  • Nehemiya 9:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Munagawa nyanja+ pamaso pawo ndipo iwo anadutsa panthaka youma pakati pa nyanja.+ Anthu amene anali kuwathamangitsa munawaponya m’nyanja yozama+ ngati mwala+ woponyedwa m’madzi amphamvu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena