Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Nthawi yomweyo Mose anatambasula dzanja lake ndi kuloza panyanja, ndipo nyanjayo inayamba kubwerera m’malo mwake, kuli pafupi kucha. Pamenepo Aiguputo anayamba kuthawa kuti madziwo asawapeze, koma Yehova anakutumulira Aiguputowo pakatikati pa nyanja.+

  • Deuteronomo 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Amenenso sanaone zimene Mulungu anachitira gulu lankhondo la Aiguputo, mahatchi* ake ndi magaleta* ake ankhondo, amene anawamiza m’madzi a m’Nyanja Yofiira pamene anali kukuthamangitsani,+ ndipo Yehova anawononga Iguputo moti ndi mmene zilili kufikira lero.+

  • Nehemiya 9:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Munagawa nyanja+ pamaso pawo ndipo iwo anadutsa panthaka youma pakati pa nyanja.+ Anthu amene anali kuwathamangitsa munawaponya m’nyanja yozama+ ngati mwala+ woponyedwa m’madzi amphamvu.+

  • Salimo 78:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Anapitiriza kuwatsogolera ndi kuwateteza ndipo iwo sanachite mantha.+

      Nyanja inamiza adani awo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena