Ekisodo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa nthawiyo Mose ndi ana a Isiraeli anayamba kuimbira Yehova nyimbo iyi, kuti:+“Ndiimbira Yehova, pakuti iye wakwezeka koposa.+Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.+ Salimo 106:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno madzi anamiza adani awo,+Moti panalibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+ Aheberi 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mwa chikhulupiriro, anthu a Mulunguwo anawoloka Nyanja Yofiira ngati kuti akudutsa pamtunda pouma,+ koma Aiguputo atalimba mtima ndi kulowa panyanjapo, nyanjayo inawamiza.+
15 Pa nthawiyo Mose ndi ana a Isiraeli anayamba kuimbira Yehova nyimbo iyi, kuti:+“Ndiimbira Yehova, pakuti iye wakwezeka koposa.+Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.+
29 Mwa chikhulupiriro, anthu a Mulunguwo anawoloka Nyanja Yofiira ngati kuti akudutsa pamtunda pouma,+ koma Aiguputo atalimba mtima ndi kulowa panyanjapo, nyanjayo inawamiza.+