Ekisodo 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo pamene amuna anali kuimba, Miriamu anathirira mang’ombe kuti:+ “Imbirani Yehova+ pakuti wakwezeka koposa.+Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.”+ Salimo 136:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amenenso anakutumulira Farao ndi gulu lake lankhondo m’Nyanja Yofiira:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
21 Ndipo pamene amuna anali kuimba, Miriamu anathirira mang’ombe kuti:+ “Imbirani Yehova+ pakuti wakwezeka koposa.+Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.”+
15 Amenenso anakutumulira Farao ndi gulu lake lankhondo m’Nyanja Yofiira:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+