Oweruza 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mvetserani mafumu inu,+ inunso nduna, tcherani khutu:Ine ndidzaimbira Yehova, ndithu ndidzamuimbira.Ndidzaimbira Yehova, Mulungu wa Isiraeli,+ nyimbo zomutamanda.+
3 Mvetserani mafumu inu,+ inunso nduna, tcherani khutu:Ine ndidzaimbira Yehova, ndithu ndidzamuimbira.Ndidzaimbira Yehova, Mulungu wa Isiraeli,+ nyimbo zomutamanda.+