Ekisodo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndi kumuuza kuti:+ “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Lolani anthu anga apite m’chipululu kuti akachite chikondwerero.’”+ Ekisodo 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ine ndine Yehova Mulungu wako,+ amene ndinakutulutsa m’dziko la Iguputo, m’nyumba yaukapolo.+
5 Kenako Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndi kumuuza kuti:+ “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Lolani anthu anga apite m’chipululu kuti akachite chikondwerero.’”+