Ekisodo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Mose anati: “Tipita ndi achinyamata athu ndi achikulire omwe. Tipita ndi ana athu aamuna ndi ana athu aakazi+ pamodzi ndi nkhosa ndi ng’ombe zathu,+ chifukwa tikukachitira Yehova chikondwerero.”+
9 Pamenepo Mose anati: “Tipita ndi achinyamata athu ndi achikulire omwe. Tipita ndi ana athu aamuna ndi ana athu aakazi+ pamodzi ndi nkhosa ndi ng’ombe zathu,+ chifukwa tikukachitira Yehova chikondwerero.”+