2 Samueli 22:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 N’chifukwa chake ndidzayamika inu Yehova pakati pa mitundu.+Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+ Salimo 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzatamanda Yehova chifukwa cha chilungamo chake.+Ndidzaimba nyimbo motsatizana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda dzina+ la Yehova Wam’mwambamwamba.+
50 N’chifukwa chake ndidzayamika inu Yehova pakati pa mitundu.+Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+
17 Ndidzatamanda Yehova chifukwa cha chilungamo chake.+Ndidzaimba nyimbo motsatizana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda dzina+ la Yehova Wam’mwambamwamba.+