Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 35:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Lilime langa linene chapansipansi za chilungamo chanu,+

      Ndipo likutamandeni tsiku lonse.+

  • Salimo 51:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Inu Mulungu, ndilanditseni ku mlandu wa magazi,+ inu Mulungu wa chipulumutso changa,+

      Kuti lilime langa linene za chilungamo chanu mokondwera.+

  • Salimo 71:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakamwa panga padzanena za chilungamo chanu,+

      Padzanena za chipulumutso chanu tsiku lonse,+

      Pakuti ntchito za chilungamo ndi chipulumutso chanu ndi zochuluka ndipo sindinathe kuziwerenga.+

  • Salimo 98:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Yehova wachititsa chipulumutso chake kudziwika.+

      Chilungamo chake wachisonyeza ku mitundu ya anthu.+

  • Salimo 145:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Iwo adzalankhula mosefukira za kuchuluka kwa ubwino wanu,+

      Ndipo adzafuula mokondwera chifukwa cha chilungamo chanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena