Salimo 38:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Fulumirani kundithandiza,+Inu Yehova, chipulumutso changa.+ Salimo 88:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 88 Inu Yehova, Mulungu wa chipulumutso changa,+Masana ndimafuula kwa inu,+Usikunso ndimafuula pamaso panu.+ Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+ Chivumbulutso 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anapitirizabe kufuula ndi mawu okweza, kuti: “Chipulumutso chathu chachokera kwa Mulungu wathu,+ amene wakhala pampando wachifumu,+ ndi kwa Mwanawankhosa.”+
88 Inu Yehova, Mulungu wa chipulumutso changa,+Masana ndimafuula kwa inu,+Usikunso ndimafuula pamaso panu.+
2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+
10 Iwo anapitirizabe kufuula ndi mawu okweza, kuti: “Chipulumutso chathu chachokera kwa Mulungu wathu,+ amene wakhala pampando wachifumu,+ ndi kwa Mwanawankhosa.”+