Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 49:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndithu ndidzayembekezera chipulumutso kwa inu, Yehova.+

  • Salimo 27:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Musandibisire nkhope yanu.+

      Musabweze mtumiki wanu mutakwiya.+

      Inu mukhale mthandizi wanga.+

      Musanditaye ndi kundisiya, inu Mulungu wa chipulumutso changa.+

  • Salimo 51:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Inu Mulungu, ndilanditseni ku mlandu wa magazi,+ inu Mulungu wa chipulumutso changa,+

      Kuti lilime langa linene za chilungamo chanu mokondwera.+

  • Salimo 68:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Adalitsike Yehova, amene amanyamula katundu wathu tsiku ndi tsiku,+

      Mulungu woona wa chipulumutso chathu.+ [Seʹlah.]

  • Yesaya 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+

  • Luka 1:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Ndipo mzimu wanga sungaleke kusefukira+ ndi chimwemwe mwa Mulungu, Mpulumutsi wanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena