Salimo 55:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Umutulire Yehova nkhawa zako,+Ndipo iye adzakuchirikiza.+Sadzalola kuti wolungama agwedezeke.+ 1 Petulo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chitani zimenezi pamene mukumutulira nkhawa zanu zonse,+ pakuti amakuderani nkhawa.+